Deuteronomo 32:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndikanoladi lupanga langa lonyezimira,+Dzanja langa likagwira chiweruzo,+Ndidzalipsira adani anga,+Ndipo ndidzabwezera chilango kwa odana nane kwambiri.+ Yeremiya 47:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Eyaa! iwe lupanga la Yehova.+ Kodi sukhala chete kufikira liti? Bwerera m’chimake.+ Pumula, ndipo ukhale chete.
41 Ndikanoladi lupanga langa lonyezimira,+Dzanja langa likagwira chiweruzo,+Ndidzalipsira adani anga,+Ndipo ndidzabwezera chilango kwa odana nane kwambiri.+
6 “Eyaa! iwe lupanga la Yehova.+ Kodi sukhala chete kufikira liti? Bwerera m’chimake.+ Pumula, ndipo ukhale chete.