Yeremiya 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pa nthawiyo adzauza anthu awa ndi Yerusalemu kuti: “M’njira zodutsidwadutsidwa za m’chipululu zopita kwa mwana wamkazi wa anthu anga+ mukutuluka mphepo yotentha.+ Mphepo imeneyi si youluzira mankhusu* kapena yoyeretsera tirigu. Ezekieli 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ndidzatumiza mphepo yamkuntho, mvula yambiri ndi matalala, kusonyeza mkwiyo wanga kuti ndikuwonongeni.+
11 Pa nthawiyo adzauza anthu awa ndi Yerusalemu kuti: “M’njira zodutsidwadutsidwa za m’chipululu zopita kwa mwana wamkazi wa anthu anga+ mukutuluka mphepo yotentha.+ Mphepo imeneyi si youluzira mankhusu* kapena yoyeretsera tirigu.
13 “Chotero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ndidzatumiza mphepo yamkuntho, mvula yambiri ndi matalala, kusonyeza mkwiyo wanga kuti ndikuwonongeni.+