2 Mbiri 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anabwera ndi magaleta 1,200+ ndi amuna okwera pamahatchi 60,000. Anabweranso ndi anthu osawerengeka+ kuchokera ku Iguputo. Anthuwo anali Alibiya,+ Asuki ndi Aitiyopiya.+ Yesaya 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Yehova anati: “Monga momwe mtumiki wanga Yesaya wayendera wopanda zovala ndiponso wopanda nsapato kwa zaka zitatu, kuti akhale chizindikiro+ ndi chenjezo kwa Iguputo+ ndi Itiyopiya,+
3 Anabwera ndi magaleta 1,200+ ndi amuna okwera pamahatchi 60,000. Anabweranso ndi anthu osawerengeka+ kuchokera ku Iguputo. Anthuwo anali Alibiya,+ Asuki ndi Aitiyopiya.+
3 Kenako Yehova anati: “Monga momwe mtumiki wanga Yesaya wayendera wopanda zovala ndiponso wopanda nsapato kwa zaka zitatu, kuti akhale chizindikiro+ ndi chenjezo kwa Iguputo+ ndi Itiyopiya,+