2 Mafumu 19:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Chifukwa kundipsera mtima kwako+ ndi kufuula kwako zafika m’makutu mwanga,+Ndithu ndidzakola mphuno yako ndi ngowe yanga, ndipo ndidzamanga zingwe zanga pakamwa pako.+Kenako ndidzakukoka n’kukubweza kudzera njira imene unadutsa pobwera.”+ Salimo 32:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthu inu, musakhale ngati hatchi kapena nyulu* yosazindikira,+Imene munthu amachita kuimanga chingwe chapakamwa ndi chapamutu kuti athetse kupulupudza kwake,+Ndi kuti aiyandikire.”+
28 Chifukwa kundipsera mtima kwako+ ndi kufuula kwako zafika m’makutu mwanga,+Ndithu ndidzakola mphuno yako ndi ngowe yanga, ndipo ndidzamanga zingwe zanga pakamwa pako.+Kenako ndidzakukoka n’kukubweza kudzera njira imene unadutsa pobwera.”+
9 Anthu inu, musakhale ngati hatchi kapena nyulu* yosazindikira,+Imene munthu amachita kuimanga chingwe chapakamwa ndi chapamutu kuti athetse kupulupudza kwake,+Ndi kuti aiyandikire.”+