Yesaya 9:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti goli la katundu wawo,+ ndodo yomwe inali pamapewa awo, ndiponso ndodo ya amene anali kuwakusira ku ntchito,+ mwazithyolathyola ngati pa tsiku limene Amidiyani anagonjetsedwa.+ Yesaya 37:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndiyeno mngelo+ wa Yehova anapita kumsasa wa Asuri n’kukapha asilikali 185,000.+ Anthu podzuka m’mawa, anangoona kuti onse aja ndi mitembo yokhayokha.+
4 Pakuti goli la katundu wawo,+ ndodo yomwe inali pamapewa awo, ndiponso ndodo ya amene anali kuwakusira ku ntchito,+ mwazithyolathyola ngati pa tsiku limene Amidiyani anagonjetsedwa.+
36 Ndiyeno mngelo+ wa Yehova anapita kumsasa wa Asuri n’kukapha asilikali 185,000.+ Anthu podzuka m’mawa, anangoona kuti onse aja ndi mitembo yokhayokha.+