2 Samueli 23:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Munthu akamazigwiraAyenera kukhala ndi zida zachitsulo ndi mkondo,Ndipo zidzatenthedwa ndi moto n’kupseratu.”+ Yesaya 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti kuipa kwayaka ngati moto,+ ndipo kudzanyeketsa zitsamba zaminga ndi udzu.+ Kuipako kudzayaka m’zitsamba zowirira za m’nkhalango,+ ndipo utsi wa mitengoyo udzakwera m’mwamba kuti tolo!+
7 Munthu akamazigwiraAyenera kukhala ndi zida zachitsulo ndi mkondo,Ndipo zidzatenthedwa ndi moto n’kupseratu.”+
18 Pakuti kuipa kwayaka ngati moto,+ ndipo kudzanyeketsa zitsamba zaminga ndi udzu.+ Kuipako kudzayaka m’zitsamba zowirira za m’nkhalango,+ ndipo utsi wa mitengoyo udzakwera m’mwamba kuti tolo!+