Yesaya 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndaleka kumukwiyira.+ Munthu wina akaika zitsamba zaminga ndi udzu pamaso panga,+ ndidzazipondaponda ndi kuzitentha nthawi imodzi ndipo ndidzamenyana naye.+ Mateyu 13:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Chotero, monga momwe amasonkhanitsira namsongole ndi kumutentha pamoto, zidzakhalanso choncho pa mapeto a nthawi* ino.+ Yohane 15:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ngati munthu sakhala wolumikizika kwa ine, amaponyedwa kunja monga nthambi ndipo amauma. Nthambi zoterozo anthu amazisonkhanitsa ndi kuziponya pamoto ndipo zimapsa.+ Aheberi 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma ikatulutsa minga ndi mitula, imakanidwa ndipo imatsala pang’ono kutembereredwa.+ Mapeto ake imatenthedwa.+
4 Ndaleka kumukwiyira.+ Munthu wina akaika zitsamba zaminga ndi udzu pamaso panga,+ ndidzazipondaponda ndi kuzitentha nthawi imodzi ndipo ndidzamenyana naye.+
40 Chotero, monga momwe amasonkhanitsira namsongole ndi kumutentha pamoto, zidzakhalanso choncho pa mapeto a nthawi* ino.+
6 Ngati munthu sakhala wolumikizika kwa ine, amaponyedwa kunja monga nthambi ndipo amauma. Nthambi zoterozo anthu amazisonkhanitsa ndi kuziponya pamoto ndipo zimapsa.+
8 Koma ikatulutsa minga ndi mitula, imakanidwa ndipo imatsala pang’ono kutembereredwa.+ Mapeto ake imatenthedwa.+