Yesaya 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehova akuwabweretsera+ Mtsinje*+ wa madzi ambiri ndi amphamvu, womwe ndi mfumu ya Asuri+ ndi ulemerero wake wonse.+ Iyo idzadzaza timitsinje take tonse n’kusefukira mpaka m’mphepete mwa mitsinje yake yonse, Yesaya 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Eya! Msuri+ ndiye ndodo ya mkwiyo wanga+ komanso chikwapu chosonyezera ukali wanga chimene chili m’dzanja lake.
7 Yehova akuwabweretsera+ Mtsinje*+ wa madzi ambiri ndi amphamvu, womwe ndi mfumu ya Asuri+ ndi ulemerero wake wonse.+ Iyo idzadzaza timitsinje take tonse n’kusefukira mpaka m’mphepete mwa mitsinje yake yonse,
5 “Eya! Msuri+ ndiye ndodo ya mkwiyo wanga+ komanso chikwapu chosonyezera ukali wanga chimene chili m’dzanja lake.