2 Mafumu 19:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwo anamuuza kuti: “Hezekiya wanena kuti, ‘Lero ndi tsiku la zowawa+ ndi lodzudzula,+ tsiku la mnyozo ndi mwano.+ Tili ngati mkazi amene watsala pang’ono kubereka,+ koma alibe mphamvu zoti aberekere.+ Yesaya 26:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chifukwa cha inu Yehova, ife takhala ngati mkazi wapakati amene watsala pang’ono kubereka, amene akumva zowawa za pobereka, amene akulira ndi ululu wa pobereka.+
3 Iwo anamuuza kuti: “Hezekiya wanena kuti, ‘Lero ndi tsiku la zowawa+ ndi lodzudzula,+ tsiku la mnyozo ndi mwano.+ Tili ngati mkazi amene watsala pang’ono kubereka,+ koma alibe mphamvu zoti aberekere.+
17 Chifukwa cha inu Yehova, ife takhala ngati mkazi wapakati amene watsala pang’ono kubereka, amene akumva zowawa za pobereka, amene akulira ndi ululu wa pobereka.+