Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 28:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Udzatumikira adani ako+ amene Yehova adzawatuma kuti akuukire. Udzawatumikira uli ndi njala,+ ludzu, usiwa ndiponso ukusowa china chilichonse. Adzakuveka goli lachitsulo m’khosi lako kufikira atakufafaniza.+

  • Salimo 22:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Mphamvu yanga yauma gwaa, ngati phale.+

      Lilime langa lamamatira kunkhama zanga,+

      Ndipo mwandikhazika m’fumbi la imfa.+

  • Maliro 4:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Lilime la ana oyamwa lamamatira kummero chifukwa cha ludzu.+

      Ana apempha chakudya+ koma palibe amene akuwapatsa.+

  • Luka 16:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Choncho anaitana kuti, ‘Atate Abulahamu,+ ndichitireni chifundo. Mutume Lazaro kuti aviike nsonga ya chala chake m’madzi kuti aziziritse lilime langa,+ chifukwa ndikuzunzika m’moto wolilimawu.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena