Deuteronomo 33:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mulungu anakhala mfumu mu Yesuruni,*+Pamene atsogoleri a anthu anasonkhana pamodzi,+Chiwerengero chonse cha mafuko a Isiraeli.+ Yesaya 49:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Amene akukuzunza ndidzawachititsa kuti adye mnofu wawo womwe, ndipo adzaledzera ndi magazi awo omwe ngati kuti amwa vinyo wotsekemera. Anthu onse ndithu adzadziwa kuti ine, Yehova,+ ndine Mpulumutsi wako+ ndiponso Wokuwombola,+ Wamphamvu wa Yakobo.”+ Yesaya 60:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iwe udzayamwa mkaka wa mitundu ya anthu,+ ndipo udzayamwa bere la mafumu.+ Udzadziwadi kuti ine Yehova+ ndine Mpulumutsi wako,+ ndipo Wamphamvu+ wa Yakobo ndiye Wokuwombola.+
5 Mulungu anakhala mfumu mu Yesuruni,*+Pamene atsogoleri a anthu anasonkhana pamodzi,+Chiwerengero chonse cha mafuko a Isiraeli.+
26 Amene akukuzunza ndidzawachititsa kuti adye mnofu wawo womwe, ndipo adzaledzera ndi magazi awo omwe ngati kuti amwa vinyo wotsekemera. Anthu onse ndithu adzadziwa kuti ine, Yehova,+ ndine Mpulumutsi wako+ ndiponso Wokuwombola,+ Wamphamvu wa Yakobo.”+
16 Iwe udzayamwa mkaka wa mitundu ya anthu,+ ndipo udzayamwa bere la mafumu.+ Udzadziwadi kuti ine Yehova+ ndine Mpulumutsi wako,+ ndipo Wamphamvu+ wa Yakobo ndiye Wokuwombola.+