Salimo 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova amadziwika ndi ziweruzo zimene amapereka.+Woipa wakodwa mumsampha wa ntchito ya manja ake.+Higayoni.* [Seʹlah.] Salimo 58:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo mtundu wa anthu udzati:+ “Ndithudi wolungama adzalandira mphoto.+Ndithudi pali Mulungu amene akuweruza dziko lapansi.”+ Ezekieli 39:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “‘Iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wawo, ndikadzawapititsa kumayiko ena n’kuwabwezanso kudziko lawo onse pamodzi.+ Kumayikowo ndidzatengako Aisiraeli onse moti sindidzasiyako aliyense.+
16 Yehova amadziwika ndi ziweruzo zimene amapereka.+Woipa wakodwa mumsampha wa ntchito ya manja ake.+Higayoni.* [Seʹlah.]
11 Ndipo mtundu wa anthu udzati:+ “Ndithudi wolungama adzalandira mphoto.+Ndithudi pali Mulungu amene akuweruza dziko lapansi.”+
28 “‘Iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wawo, ndikadzawapititsa kumayiko ena n’kuwabwezanso kudziko lawo onse pamodzi.+ Kumayikowo ndidzatengako Aisiraeli onse moti sindidzasiyako aliyense.+