Yesaya 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 amene anachititsa nthaka kukhala ngati chipululu, amene anagonjetsa mizinda ya padziko lapansi,+ ndiponso amene sanali kutsegulira njira akaidi ake kuti azipita kwawo?’+ Yesaya 45:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ine ndidzakhala kutsogolo kwako+ ndipo ndidzasalaza zitunda za m’dzikolo.+ Ndidzaphwanyaphwanya zitseko zamkuwa ndipo ndidzadula mipiringidzo yachitsulo.+
17 amene anachititsa nthaka kukhala ngati chipululu, amene anagonjetsa mizinda ya padziko lapansi,+ ndiponso amene sanali kutsegulira njira akaidi ake kuti azipita kwawo?’+
2 “Ine ndidzakhala kutsogolo kwako+ ndipo ndidzasalaza zitunda za m’dzikolo.+ Ndidzaphwanyaphwanya zitseko zamkuwa ndipo ndidzadula mipiringidzo yachitsulo.+