2 Mafumu 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mfumu ya Babuloyo inapha anthuwo+ ku Ribila m’dziko la Hamati.+ Choncho Ayuda anachoka kudziko lawo n’kupita ku ukapolo.+ Yesaya 64:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mizinda yanu yoyera+ yasanduka chipululu. Ziyoni+ wangosanduka chipululu basi, ndipo Yerusalemu wasanduka bwinja.+
21 Mfumu ya Babuloyo inapha anthuwo+ ku Ribila m’dziko la Hamati.+ Choncho Ayuda anachoka kudziko lawo n’kupita ku ukapolo.+
10 Mizinda yanu yoyera+ yasanduka chipululu. Ziyoni+ wangosanduka chipululu basi, ndipo Yerusalemu wasanduka bwinja.+