Ekisodo 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 ndipo mwana aliyense woyamba kubadwa+ m’dziko la Iguputo adzafa. Kuyambira mwana woyamba wa Farao, amene wakhala pampando wachifumu, mpaka mwana woyamba wa kapolo wamkazi wokhala pamphero ndiponso mwana woyamba kubadwa wa nyama iliyonse.+ Mateyu 24:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Akazi awiri adzakhala akupera pamphero+ wina adzatengedwa ndipo winayo adzasiyidwa.+
5 ndipo mwana aliyense woyamba kubadwa+ m’dziko la Iguputo adzafa. Kuyambira mwana woyamba wa Farao, amene wakhala pampando wachifumu, mpaka mwana woyamba wa kapolo wamkazi wokhala pamphero ndiponso mwana woyamba kubadwa wa nyama iliyonse.+