Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 23:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti iye amadziwa bwino njira imene ine ndimadutsa.+

      Akamaliza kundiyesa, ndidzakhala ngati golide.+

  • Miyambo 17:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Siliva amamuyengera m’mbiya yoyengera ndipo golide amamuyengera m’ng’anjo,+ koma Yehova ndiye amene amayesa mitima.+

  • Malaki 3:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Iye adzakhala pansi ngati woyenga zitsulo ndiponso ngati woyeretsa siliva.+ Adzayeretsa ana a Levi+ ndipo adzawayeretsa ngati golide+ ndi siliva. Pamene azidzapereka nsembe zawo ngati mphatso, Yehova adzaona kuti nsembe zawozo akuzipereka+ molungama.

  • Aheberi 12:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Zoonadi, palibe chilango chimene chimamveka chosangalatsa pa nthawi yomwe ukuchilandira, koma chimakhala chowawa.+ Komabe pambuyo pake, kwa anthu amene aphunzirapo kanthu pa chilangocho, chimabala chipatso chamtendere,+ chomwe ndi chilungamo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena