Yesaya 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Iye adzameza imfa kwamuyaya+ ndipo Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzapukuta misozi pankhope zonse za anthu.+ Adzachotsa kunyozeka kwa anthu ake padziko lonse lapansi,+ pakuti Yehova ndiye wanena zimenezi. Yesaya 65:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndidzasangalala ndi Yerusalemu ndipo ndidzakondwera ndi anthu anga.+ Mwa iye simudzamvekanso kulira kokweza mawu kapena kulira kwachisoni.”+
8 Iye adzameza imfa kwamuyaya+ ndipo Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzapukuta misozi pankhope zonse za anthu.+ Adzachotsa kunyozeka kwa anthu ake padziko lonse lapansi,+ pakuti Yehova ndiye wanena zimenezi.
19 Ndidzasangalala ndi Yerusalemu ndipo ndidzakondwera ndi anthu anga.+ Mwa iye simudzamvekanso kulira kokweza mawu kapena kulira kwachisoni.”+