Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Hoseya 13:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Ine ndidzawawombola ku Manda*+ ndiponso ku imfa.+ Iwe Imfa amene umabweretsa ululu woopsa, kodi mphamvu yako ili kuti?+ Iwe Manda amene umawononga, kodi uli kuti?+ Koma Efuraimu sindimumverabe chisoni.+

  • 1 Akorinto 15:54
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 54 Koma chokhoza kuwonongekachi chikadzavala kusawonongeka, ndipo chokhoza kufachi chikadzavala kusafa, pamenepo adzakwaniritsidwa mawu amene analembedwa kuti: “Imfa+ yamezedwa kwamuyaya.”+

  • 2 Timoteyo 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Koma tsopano izi zatsimikizirika bwino chifukwa cha kuonekera+ kwa Mpulumutsi wathu Khristu Yesu, amene wathetsa mphamvu imfa.+ Kudzera mu uthenga wabwino,+ iye watidziwitsa bwinobwino+ mmene tingapezere moyo+ wosawonongeka.+

  • Aheberi 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Anachitanso zimenezi kuti amasule+ onse amene poopa imfa,+ anali mu ukapolo moyo wawo wonse.+

  • Chivumbulutso 20:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndipo imfa+ ndi Manda zinaponyedwa m’nyanja yamoto.+ Nyanja yamoto imeneyi ikuimira imfa yachiwiri.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena