Salimo 119:176 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 176 Ndayendayenda ngati nkhosa yosochera.+ Ndifunefuneni ine mtumiki wanu,+Pakuti sindinaiwale malamulo anu.+ Ezekieli 34:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nkhosa zanga+ zinasochera m’mapiri onse ndi m’zitunda zonse zitalizitali.+ Zinabalalika padziko lonse lapansi, ndipo panalibe wozifufuza ndi kuziyang’anayang’ana. 1 Petulo 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pakuti munali ngati nkhosa zosochera,+ koma tsopano mwabwerera kwa m’busa+ wanu ndi woyang’anira miyoyo yanu.
176 Ndayendayenda ngati nkhosa yosochera.+ Ndifunefuneni ine mtumiki wanu,+Pakuti sindinaiwale malamulo anu.+
6 Nkhosa zanga+ zinasochera m’mapiri onse ndi m’zitunda zonse zitalizitali.+ Zinabalalika padziko lonse lapansi, ndipo panalibe wozifufuza ndi kuziyang’anayang’ana.
25 Pakuti munali ngati nkhosa zosochera,+ koma tsopano mwabwerera kwa m’busa+ wanu ndi woyang’anira miyoyo yanu.