6 Yehova wa makamu adzakonzera anthu a mitundu yonse+ m’phiri ili,+ phwando la zakudya zabwinozabwino,+ phwando la vinyo wokoma kwambiri, phwando la zakudya zabwinozabwino zokhala ndi mafuta a m’mafupa,+ ndiponso la vinyo+ wokoma kwambiri, wosefedwa bwino.+