Ezekieli 33:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “‘Koma mlondayo akaona lupanga likubwera, iye osaliza lipenga,+ anthu osamva chenjezo lililonse, lupangalo n’kufika ndi kupha anthu, anthuwo adzaphedwa chifukwa cha zolakwa zawo,+ koma magazi awo ndidzawafuna kuchokera m’manja mwa mlondayo.’+
6 “‘Koma mlondayo akaona lupanga likubwera, iye osaliza lipenga,+ anthu osamva chenjezo lililonse, lupangalo n’kufika ndi kupha anthu, anthuwo adzaphedwa chifukwa cha zolakwa zawo,+ koma magazi awo ndidzawafuna kuchokera m’manja mwa mlondayo.’+