Yesaya 56:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Alonda ake ndi akhungu+ ndipo sakudziwa chilichonse.+ Onsewo ndi agalu opanda mawu. Satha kuuwa.+ Amangokhalira kupuma wefuwefu ndi kugona pansi. Amakonda kugona tulo.+
10 Alonda ake ndi akhungu+ ndipo sakudziwa chilichonse.+ Onsewo ndi agalu opanda mawu. Satha kuuwa.+ Amangokhalira kupuma wefuwefu ndi kugona pansi. Amakonda kugona tulo.+