Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 6:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ukachititse anthu awa kuumitsa mtima wawo,+ ndipo ukachititse makutu awo kuti asamamve.+ Ukamate maso awo kuti asamaone ndi maso awowo, ndiponso kuti asamamve ndi makutu awo, komanso kuti mtima wawo usamvetsetse zinthu, kuti angatembenuke n’kuchira.”+

  • Yesaya 29:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pakuti Yehova wakukhuthulirani mzimu wa tulo tatikulu+ ndipo watseka maso anu, omwe ndi aneneri.+ Waphimba mitu yanu,+ imene ndi anthu amasomphenya.+

  • Mateyu 15:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Alekeni amenewo. Iwo ndi atsogoleri akhungu. Chotero ngati munthu wakhungu akutsogolera wakhungu mnzake, onse awiri adzagwera m’dzenje.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena