Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 69:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Maso awo achite mdima kuti asaone,+

      Ndipo chititsani miyendo* yawo kunjenjemera mosalekeza.+

  • Yesaya 6:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ukachititse anthu awa kuumitsa mtima wawo,+ ndipo ukachititse makutu awo kuti asamamve.+ Ukamate maso awo kuti asamaone ndi maso awowo, ndiponso kuti asamamve ndi makutu awo, komanso kuti mtima wawo usamvetsetse zinthu, kuti angatembenuke n’kuchira.”+

  • Machitidwe 28:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Pakuti anthu awa aumitsa mtima wawo, ndipo amva ndi makutu awo koma osalabadira. Iwo atseka maso awo, kuti asaone ndi maso awo, asamve ndi makutu awo ndi kuti asazindikire ndi mtima wawo n’kutembenuka kuti ine ndiwachiritse.”’+

  • Aroma 11:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 monga mmene Malemba amanenera kuti: “Mulungu wawapatsa mzimu wa tulo tatikulu,+ maso osaona ndi makutu osatha kumva, kufikira lero.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena