Salimo 55:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Inu Mulungu, mvetserani pemphero langa.+Musanyalanyaze pempho langa lakuti mundikomere mtima.+ Salimo 71:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mundilanditse chifukwa cha chilungamo chanu ndipo mundipulumutse.+Tcherani khutu lanu kwa ine ndi kundipulumutsa.+ Salimo 116:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 116 Mtima wanga ndi wodzaza ndi chikondi, chifukwa Yehova amamva+Mawu anga ndi madandaulo anga.+
2 Mundilanditse chifukwa cha chilungamo chanu ndipo mundipulumutse.+Tcherani khutu lanu kwa ine ndi kundipulumutsa.+