Yesaya 38:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndikungokhalira kulira ngati namzeze* kapena pumbwa.*+Ndikungokhalira kubuula ngati njiwa.+ Maso anga akupenyetsetsa kumwamba motopa. Choncho ndinati:+‘Inu Yehova ine ndapanikizika. Chonde ndithandizeni.’+
14 Ndikungokhalira kulira ngati namzeze* kapena pumbwa.*+Ndikungokhalira kubuula ngati njiwa.+ Maso anga akupenyetsetsa kumwamba motopa. Choncho ndinati:+‘Inu Yehova ine ndapanikizika. Chonde ndithandizeni.’+