Yesaya 59:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tonsefe tikungolira ngati zimbalangondo ndipo tikungokhalira kubuula momvetsa chisoni ngati njiwa.+ Tinali kuyembekezera chilungamo+ koma sichinabwere. Tinali kuyembekezera chipulumutso koma chakhala nafe kutali.+ Ezekieli 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Anthu awo opulumuka adzathawa+ ndipo adzakhala pamapiri ngati njiwa za m’zigwa,+ aliyense akulira chifukwa cha zolakwa zake. Nahumu 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Nkhani imeneyi yatsimikiziridwa. Mzindawo udzavulidwa ndi kuchititsidwa manyazi, ndipo anthu ake adzatengedwa.+ Akapolo ake aakazi adzakhala akulira ngati nkhunda+ ndipo adzadziguguda pachifuwa.+
11 Tonsefe tikungolira ngati zimbalangondo ndipo tikungokhalira kubuula momvetsa chisoni ngati njiwa.+ Tinali kuyembekezera chilungamo+ koma sichinabwere. Tinali kuyembekezera chipulumutso koma chakhala nafe kutali.+
16 Anthu awo opulumuka adzathawa+ ndipo adzakhala pamapiri ngati njiwa za m’zigwa,+ aliyense akulira chifukwa cha zolakwa zake.
7 Nkhani imeneyi yatsimikiziridwa. Mzindawo udzavulidwa ndi kuchititsidwa manyazi, ndipo anthu ake adzatengedwa.+ Akapolo ake aakazi adzakhala akulira ngati nkhunda+ ndipo adzadziguguda pachifuwa.+