Salimo 85:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndithudi, chipulumutso chake chili pafupi ndi amene amamuopa,+Kuti ulemerero ukhale m’dziko lathu.+ Salimo 119:155 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 155 Chipulumutso chili kutali ndi anthu oipa,+Pakuti sanaphunzire malamulo anu ndi kuwasunga.+
9 Ndithudi, chipulumutso chake chili pafupi ndi amene amamuopa,+Kuti ulemerero ukhale m’dziko lathu.+