Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 38:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndikungokhalira kulira ngati namzeze* kapena pumbwa.*+

      Ndikungokhalira kubuula ngati njiwa.+

      Maso anga akupenyetsetsa kumwamba motopa. Choncho ndinati:+

      ‘Inu Yehova ine ndapanikizika. Chonde ndithandizeni.’+

  • Yesaya 59:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Tonsefe tikungolira ngati zimbalangondo ndipo tikungokhalira kubuula momvetsa chisoni ngati njiwa.+ Tinali kuyembekezera chilungamo+ koma sichinabwere. Tinali kuyembekezera chipulumutso koma chakhala nafe kutali.+

  • Nahumu 2:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Nkhani imeneyi yatsimikiziridwa. Mzindawo udzavulidwa ndi kuchititsidwa manyazi, ndipo anthu ake adzatengedwa.+ Akapolo ake aakazi adzakhala akulira ngati nkhunda+ ndipo adzadziguguda pachifuwa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena