Salimo 99:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kwezani Yehova Mulungu wathu+ ndipo muweramireni pachopondapo mapazi ake.+Iye ndi woyera.+ Salimo 132:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tiyeni tilowe m’chihema chake chachikulu.+Tiyeni tiwerame pachopondapo mapazi ake.+