Genesis 35:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Dziko limene ndinalipereka kwa Abulahamu ndi Isaki, ndidzalipereka kwa iwe ndi kwa mbewu yako+ yobwera pambuyo pako.”+ Yesaya 60:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anthu ako onse adzakhala olungama.+ Iwo adzakhala m’dzikomo mpaka kalekale.+ Anthuwo adzakhala mmera wobzalidwa ndi ine+ ndiponso ntchito ya manja anga,+ kuti ineyo ndikongoletsedwe.+ Ezekieli 36:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma inu mapiri a Isiraeli, mudzatulutsa nthambi ndi kubalira zipatso anthu anga Aisiraeli,+ chifukwa chakuti atsala pang’ono kulowa m’dziko lino.+ Obadiya 17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Anthu onse opulumuka adzakhala m’phiri la Ziyoni+ ndipo phiri limeneli lidzakhala loyera.+ A nyumba ya Yakobo adzatenga zinthu zoyeneradi kukhala zawo.+
12 Dziko limene ndinalipereka kwa Abulahamu ndi Isaki, ndidzalipereka kwa iwe ndi kwa mbewu yako+ yobwera pambuyo pako.”+
21 Anthu ako onse adzakhala olungama.+ Iwo adzakhala m’dzikomo mpaka kalekale.+ Anthuwo adzakhala mmera wobzalidwa ndi ine+ ndiponso ntchito ya manja anga,+ kuti ineyo ndikongoletsedwe.+
8 Koma inu mapiri a Isiraeli, mudzatulutsa nthambi ndi kubalira zipatso anthu anga Aisiraeli,+ chifukwa chakuti atsala pang’ono kulowa m’dziko lino.+
17 “Anthu onse opulumuka adzakhala m’phiri la Ziyoni+ ndipo phiri limeneli lidzakhala loyera.+ A nyumba ya Yakobo adzatenga zinthu zoyeneradi kukhala zawo.+