Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Rute 4:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Tsopano, kale mu Isiraeli munali mwambo wokhudza ufulu wowombola ndiponso wokhudza kusinthana ufuluwo, pofuna kuti atsimikizirane chilichonse. Mwambo wake unali wotere: Munthu anali kuvula nsapato+ yake ndi kuipereka kwa mnzake. Uwu ndiwo unali umboni wotsimikizirana mu Isiraeli.

  • Yesaya 8:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndikufuna mboni zokhulupirika kuti zindichitire umboni.+ Mbonizo zikhale wansembe Uriya+ ndi Zekariya mwana wa Yeberekiya.”

  • Danieli 12:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 “Koma iwe Danieli, sunga mawuwa mwachinsinsi ndipo utseke ndi kumata bukuli+ kufikira nthawi yamapeto.+ Anthu ambiri adzayenda uku ndi uku ndipo adzadziwa zinthu zambiri zoona.”+

  • Chivumbulutso 5:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Kenako, ndinaona mpukutu wolembedwa mkati ndi kunja komwe,+ uli m’dzanja lamanja la Iye wokhala pampando wachifumu.+ Unali womatidwa+ mwamphamvu ndi zidindo 7 zomatira.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena