Yesaya 30:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Yehova adzapangitsa kuti ulemerero wa mawu ake+ umveke. Adzapangitsa kuti dzanja lake limene likutsika lionekere.+ Dzanjalo lidzatsika ndi mkwiyo waukulu,+ lawi la moto wowononga,+ mvula yamphamvu ndiponso yamkuntho+ ndi matalala.+ Yesaya 30:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chifukwa cha mawu a Yehova, dziko la Asuri lidzagwidwa ndi mantha,+ ndipo iye adzalimenya ndi ndodo.+
30 Yehova adzapangitsa kuti ulemerero wa mawu ake+ umveke. Adzapangitsa kuti dzanja lake limene likutsika lionekere.+ Dzanjalo lidzatsika ndi mkwiyo waukulu,+ lawi la moto wowononga,+ mvula yamphamvu ndiponso yamkuntho+ ndi matalala.+
31 Chifukwa cha mawu a Yehova, dziko la Asuri lidzagwidwa ndi mantha,+ ndipo iye adzalimenya ndi ndodo.+