2 Mbiri 28:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 M’kupita kwa nthawi, Tigilati-pilenesere+ mfumu ya Asuri anabwera kudzamenyana naye. Iye anam’sautsa+ ndipo sanam’limbikitse. Hoseya 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Efuraimu anaona kudwala kwake ndipo Yuda anaona chilonda chake.+ Pamenepo Efuraimu anapita ku Asuri+ ndipo anatumiza amithenga kwa mfumu yaikulu.+ Koma mfumuyo sinathe kukuchiritsani anthu inu,+ ndipo sinathe kupoletsa chilonda chanu.+ Hoseya 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Dziko la Asuri silidzatipulumutsa.+ Ife sitidzakwera pamahatchi.+ Sitidzauzanso ntchito ya manja athu kuti: “Inu Mulungu wathu!” chifukwa inu mumachitira chifundo mwana wamasiye.’*+
20 M’kupita kwa nthawi, Tigilati-pilenesere+ mfumu ya Asuri anabwera kudzamenyana naye. Iye anam’sautsa+ ndipo sanam’limbikitse.
13 “Efuraimu anaona kudwala kwake ndipo Yuda anaona chilonda chake.+ Pamenepo Efuraimu anapita ku Asuri+ ndipo anatumiza amithenga kwa mfumu yaikulu.+ Koma mfumuyo sinathe kukuchiritsani anthu inu,+ ndipo sinathe kupoletsa chilonda chanu.+
3 Dziko la Asuri silidzatipulumutsa.+ Ife sitidzakwera pamahatchi.+ Sitidzauzanso ntchito ya manja athu kuti: “Inu Mulungu wathu!” chifukwa inu mumachitira chifundo mwana wamasiye.’*+