Miyambo 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pakuti nyumba yake imatsikira kumanda ndipo njira zake zimatsikira kwa akufa.+ Mlaliki 3:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Zonse zimapita kumalo amodzi.+ Zonse zinachokera kufumbi+ ndipo zonse zimabwerera kufumbi.+ Yesaya 26:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwo afa. Sadzakhalanso ndi moyo.+ Iwo ndi akufa+ ndipo sadzaukanso.+ Pa chifukwa chimenechi, mwawatembenukira kuti muwawononge n’cholinga choti asadzatchulidwenso.+ Ezekieli 32:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “‘Ku Mandako, atsogoleri a anthu amphamvu adzalankhula ndi iyeyo komanso amene anali kumuthandiza.+ Onsewo adzatsikira kumanda.+ Iwo adzaphedwa ndi lupanga ndipo adzaikidwa m’manda mofanana ndi anthu osadulidwa.
14 Iwo afa. Sadzakhalanso ndi moyo.+ Iwo ndi akufa+ ndipo sadzaukanso.+ Pa chifukwa chimenechi, mwawatembenukira kuti muwawononge n’cholinga choti asadzatchulidwenso.+
21 “‘Ku Mandako, atsogoleri a anthu amphamvu adzalankhula ndi iyeyo komanso amene anali kumuthandiza.+ Onsewo adzatsikira kumanda.+ Iwo adzaphedwa ndi lupanga ndipo adzaikidwa m’manda mofanana ndi anthu osadulidwa.