Yeremiya 50:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Taonani! Nyundo yophwanyira mitundu+ ya anthu padziko lonse lapansi yathyoledwa ndipo yawonongeka.+ Taonani! Babulo wakhala chinthu chodabwitsa pakati pa mitundu ina.+ Yeremiya 51:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Ine ndikuthira nkhondo iwe+ phiri lowononga,+ amene wawononga dziko lonse lapansi.+ Ndidzatambasula dzanja langa ndi kukuthira nkhondo. Ndidzakugubuduza kukuchotsa pamatanthwe ndipo ndidzakusandutsa phiri lotenthedwa ndi moto,” watero Yehova.+
23 Taonani! Nyundo yophwanyira mitundu+ ya anthu padziko lonse lapansi yathyoledwa ndipo yawonongeka.+ Taonani! Babulo wakhala chinthu chodabwitsa pakati pa mitundu ina.+
25 “Ine ndikuthira nkhondo iwe+ phiri lowononga,+ amene wawononga dziko lonse lapansi.+ Ndidzatambasula dzanja langa ndi kukuthira nkhondo. Ndidzakugubuduza kukuchotsa pamatanthwe ndipo ndidzakusandutsa phiri lotenthedwa ndi moto,” watero Yehova.+