Yeremiya 48:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 “‘Kulira kochokera ku Hesiboni+ kudzamveka ku Eleyale+ ndi ku Yahazi.+ Kulira kochokera ku Zowari+ kudzamveka ku Horonaimu+ ndi ku Egilati-selisiya.+ Madzi a ku Nimurimu+ nawonso adzawonongedwa.
34 “‘Kulira kochokera ku Hesiboni+ kudzamveka ku Eleyale+ ndi ku Yahazi.+ Kulira kochokera ku Zowari+ kudzamveka ku Horonaimu+ ndi ku Egilati-selisiya.+ Madzi a ku Nimurimu+ nawonso adzawonongedwa.