Miyambo 27:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Monga mbalame imene ikuthawa pachisa pake,+ ndi mmenenso amakhalira munthu amene akuthawa kwawo.+ Yesaya 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Monga insa imene ikuthamangitsidwa ndiponso monga ziweto zopanda wozikusa,+ aliyense wa iwo adzatembenukira kwa anthu ake, ndipo aliyense wa iwo adzathawira kudziko lake.+ Yeremiya 48:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Ima chilili ndi kuona zimene zikuchitika m’njira, iwe mkazi wokhala ku Aroweli.+ Funsa mwamuna ndi mkazi amene akuthawa. Uwafunse kuti, ‘Chachitika n’chiyani?’+
14 Monga insa imene ikuthamangitsidwa ndiponso monga ziweto zopanda wozikusa,+ aliyense wa iwo adzatembenukira kwa anthu ake, ndipo aliyense wa iwo adzathawira kudziko lake.+
19 “Ima chilili ndi kuona zimene zikuchitika m’njira, iwe mkazi wokhala ku Aroweli.+ Funsa mwamuna ndi mkazi amene akuthawa. Uwafunse kuti, ‘Chachitika n’chiyani?’+