Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 4:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pamenepo Kaini anachoka pamaso pa Yehova+ n’kupita kukakhala kudera la kum’mawa kwa Edeni monga wothawa.

  • Ekisodo 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Patapita nthawi, Farao anaimva nkhaniyi ndipo anafuna kupha Mose.+ Koma Mose anam’thawa+ Farao ndipo anapita kukakhala kudziko la Midiyani.+ Atafika kumeneko, anakhala pachitsime.

  • 1 Samueli 27:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Koma Davide anati mumtima mwake: “Tsiku lina Sauli adzandipha ndithu. Palibe chimene ndingachite choposa kuthawira+ kudziko la Afilisiti.+ Ndiyeno Sauli adzagwa ulesi ndipo adzasiya kundifunafuna m’dziko lonse la Isiraeli.+ Pamenepo ndidzakhala nditapulumuka m’manja mwake.”

  • 1 Mafumu 19:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Choncho anadzuka ndipo anadya ndi kumwa. Atatero, anapeza mphamvu zokwanira moti anatha kuyenda masiku 40,+ usana ndi usiku, mpaka kukafika kuphiri la Mulungu woona la Horebe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena