Yesaya 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Yehova anati: “Monga momwe mtumiki wanga Yesaya wayendera wopanda zovala ndiponso wopanda nsapato kwa zaka zitatu, kuti akhale chizindikiro+ ndi chenjezo kwa Iguputo+ ndi Itiyopiya,+ Ezekieli 30:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Lupanga lidzafikadi mu Iguputo,+ ndipo ku Itiyopiya anthu adzamva ululu waukulu. Izi zidzachitika anthu akadzaphedwa mu Iguputo, chuma cha dzikolo chikadzalandidwa komanso maziko ake akadzagwetsedwa.+ Zefaniya 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Anthu amene akundichonderera, anthu anga obalalitsidwa, adzandibweretsera mphatso kuchokera kuchigawo cha mitsinje ya ku Itiyopiya.+
3 Kenako Yehova anati: “Monga momwe mtumiki wanga Yesaya wayendera wopanda zovala ndiponso wopanda nsapato kwa zaka zitatu, kuti akhale chizindikiro+ ndi chenjezo kwa Iguputo+ ndi Itiyopiya,+
4 Lupanga lidzafikadi mu Iguputo,+ ndipo ku Itiyopiya anthu adzamva ululu waukulu. Izi zidzachitika anthu akadzaphedwa mu Iguputo, chuma cha dzikolo chikadzalandidwa komanso maziko ake akadzagwetsedwa.+
10 “Anthu amene akundichonderera, anthu anga obalalitsidwa, adzandibweretsera mphatso kuchokera kuchigawo cha mitsinje ya ku Itiyopiya.+