Yesaya 30:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti akalonga ake afika ku Zowani,+ ndipo nthumwi zake zafika mpaka ku Hanesi. Ezekieli 30:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pa tsikulo, amithenga ochokera kwa ine adzakwera zombo kuti akaopseze Itiyopiya yemwe ndi wodzidalira.+ Itiyopiya adzamva ululu woopsa pa tsiku limene Iguputo adzawonongedwe, pakuti tsikulo lidzafika ndithu.’+
9 Pa tsikulo, amithenga ochokera kwa ine adzakwera zombo kuti akaopseze Itiyopiya yemwe ndi wodzidalira.+ Itiyopiya adzamva ululu woopsa pa tsiku limene Iguputo adzawonongedwe, pakuti tsikulo lidzafika ndithu.’+