Numeri 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Atapita ku Negebu,+ anakafika ku Heburoni.+ Kumeneko anapezako Ahimani, Sesai ndi Talimai,+ mbadwa za Anaki.*+ Mzinda wa Heburoni+ unamangidwa zaka 7 mzinda wa Zowani+ wa ku Iguputo usanamangidwe. Salimo 78:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mulungu anachita zodabwitsa pamaso pa makolo awo+M’dziko la Iguputo,+ m’dera la Zowani.+ Yesaya 30:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti akalonga ake afika ku Zowani,+ ndipo nthumwi zake zafika mpaka ku Hanesi. Ezekieli 30:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mzinda wa Patirosi+ ndidzausandutsa bwinja. Mzinda wa Zowani+ ndidzautentha ndi moto ndipo ndidzapereka ziweruzo mumzinda wa No.+
22 Atapita ku Negebu,+ anakafika ku Heburoni.+ Kumeneko anapezako Ahimani, Sesai ndi Talimai,+ mbadwa za Anaki.*+ Mzinda wa Heburoni+ unamangidwa zaka 7 mzinda wa Zowani+ wa ku Iguputo usanamangidwe.
14 Mzinda wa Patirosi+ ndidzausandutsa bwinja. Mzinda wa Zowani+ ndidzautentha ndi moto ndipo ndidzapereka ziweruzo mumzinda wa No.+