1 Samueli 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma mukachita zinthu zoipa mouma khosi, mudzasesedwa,+ inu pamodzi ndi mfumu yanuyo.”+ 1 Mafumu 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma inuyo ndi ana anu mukadzabwerera n’kusiya kunditsatira,+ osasunga malamulo anga amene ndakupatsani, komanso mukadzapita kukatumikira milungu ina+ ndi kuigwadira, 2 Atesalonika 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amenewa adzawaweruza kuti alandire chilango+ cha chiwonongeko chamuyaya,+ kuwachotsa pamaso pa Ambuye ndi ku ulemerero wa mphamvu zake.+
6 Koma inuyo ndi ana anu mukadzabwerera n’kusiya kunditsatira,+ osasunga malamulo anga amene ndakupatsani, komanso mukadzapita kukatumikira milungu ina+ ndi kuigwadira,
9 Amenewa adzawaweruza kuti alandire chilango+ cha chiwonongeko chamuyaya,+ kuwachotsa pamaso pa Ambuye ndi ku ulemerero wa mphamvu zake.+