Ezara 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero iwo anamanga guwa lansembe lolimba pamalo ake+ akale, chifukwa anali kuopa anthu a mitundu ina.+ Atatero anayamba kuperekerapo nsembe zopsereza kwa Yehova, zam’mawa ndi zamadzulo.+
3 Chotero iwo anamanga guwa lansembe lolimba pamalo ake+ akale, chifukwa anali kuopa anthu a mitundu ina.+ Atatero anayamba kuperekerapo nsembe zopsereza kwa Yehova, zam’mawa ndi zamadzulo.+