Yobu 19:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Amuna onse amene anali anzanga apamtima akudana nane,+Ndipo amene ndinali kuwakonda anditembenukira.+ Salimo 38:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ine ndinati: “Ngati simundiyankha adani anga adzasangalala chifukwa cha kusautsika kwanga.+Phazi langa likaterereka,+ iwo adzadzikweza pamaso panga.”+ Salimo 41:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma munthu amene ndinali kukhala naye mwamtendere, amene ndinali kumukhulupirira,+Munthu amene anali kudya chakudya changa,+ wakweza chidendene chake kundiukira.+
19 Amuna onse amene anali anzanga apamtima akudana nane,+Ndipo amene ndinali kuwakonda anditembenukira.+
16 Ine ndinati: “Ngati simundiyankha adani anga adzasangalala chifukwa cha kusautsika kwanga.+Phazi langa likaterereka,+ iwo adzadzikweza pamaso panga.”+
9 Koma munthu amene ndinali kukhala naye mwamtendere, amene ndinali kumukhulupirira,+Munthu amene anali kudya chakudya changa,+ wakweza chidendene chake kundiukira.+