Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 6:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Adani anga onse adzachita manyazi kwambiri+ ndipo adzasokonezeka.

      Adzabwerera, ndipo nthawi yomweyo adzachita manyazi.+

  • Salimo 35:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Onse amene akukondwera ndi tsoka langa,+

      Achite manyazi ndi kuthedwa nzeru.+

      Onse odzikweza pamaso panga achite manyazi+ ndi kutsitsidwa.+

  • Salimo 40:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Onse amene akufunafuna moyo wanga kuti aufafanize+

      Achite manyazi ndi kuthedwa nzeru.+

      Amene akukondwera ndi tsoka langa abwerere ndipo anyazitsidwe.+

  • Yeremiya 23:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Ndidzaika chitonzo pa inu mpaka kalekale ndipo mudzanyozeka mpaka kalekale. Zimenezi sizidzaiwalika.”’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena