Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 20:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma Yehova anali nane+ ngati msilikali wamphamvu ndi woopsa.+ N’chifukwa chake anthu amene akundizunza adzakhumudwa ndipo sadzapambana.+ Adzachita manyazi kwambiri chifukwa adzaona kuti sizinawayendere bwino. Manyazi awo adzakhala nawo mpaka kalekale ndipo sadzaiwalika.+

  • Yeremiya 24:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndidzawasandutsa chinthu chimene maufumu onse a padziko lapansi adzanthunthumira nacho, chifukwa cha masoka aakulu amene ndidzawagwetsera.+ Anthu a mitundu ina adzawatonza, kuwayesa chosereula, kuwanyoza+ ndipo adzakhala otembereredwa+ kulikonse kumene ndidzawabalalitsirako.+

  • Yeremiya 42:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “Yehova Mulungu wa makamu, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Monga mmene ndinasonyezera anthu okhala mu Yerusalemu+ mkwiyo ndi kupsa mtima kwanga, inunso ndidzakusonyezani mkwiyo wanga chifukwa chakuti mwakakhala ku Iguputo. Mudzakhala otembereredwa ndipo mudzakhala chinthu chodabwitsa ndi chotonzedwa,+ moti malo ano simudzawaonanso.’+

  • Danieli 9:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Inu Yehova, nthawi zonse mumachita zinthu zolungama.+ Chonde, chotsani mkwiyo wanu waukulu pa Yerusalemu, phiri lanu loyera.+ Pakuti chifukwa cha machimo athu ndi zolakwa za makolo athu,+ Yerusalemu ndi anthu anu takhala chinthu chotonzedwa ndi anthu onse otizungulira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena