Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 13:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pamenepo ukawauze kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Inetu ndikuledzeretsa+ anthu onse a m’dzikoli, mafumu amene akukhala pampando wa Davide,+ ansembe, aneneri ndi onse okhala mu Yerusalemu.

  • Yeremiya 17:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 pazipata za mzindawu padzalowa mafumu ndi akalonga+ okhala pampando wachifumu wa Davide.+ Mafumuwo pamodzi ndi akalonga awo adzalowa atakwera magaleta ndi mahatchi. Adzalowa pamodzi ndi anthu a mu Yuda komanso anthu okhala mu Yerusalemu ndipo mumzindawu mudzakhala anthu mpaka kalekale.

  • Luka 1:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Ameneyu adzakhala wamkulu+ ndipo adzatchedwa Mwana wa Wam’mwambamwamba.+ Yehova Mulungu adzam’patsa mpando wachifumu+ wa Davide atate wake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena