Yeremiya 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Imirira pachipata cha nyumba ya Yehova, ndi kulengeza kuti,+ ‘Tamverani mawu a Yehova nonsenu okhala mu Yuda, amene mumalowa pazipata izi kuti mukagwadire Yehova. Yeremiya 17:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndipo ukawauze kuti, ‘Tamverani mawu a Yehova inu mafumu a Yuda ndi inu nonse okhala mu Yuda komanso inu nonse okhala mu Yerusalemu amene mumalowera pazipata izi.+
2 “Imirira pachipata cha nyumba ya Yehova, ndi kulengeza kuti,+ ‘Tamverani mawu a Yehova nonsenu okhala mu Yuda, amene mumalowa pazipata izi kuti mukagwadire Yehova.
20 Ndipo ukawauze kuti, ‘Tamverani mawu a Yehova inu mafumu a Yuda ndi inu nonse okhala mu Yuda komanso inu nonse okhala mu Yerusalemu amene mumalowera pazipata izi.+