Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 49:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Mvetserani izi, anthu nonsenu.

      Tcherani khutu inu nonse a m’nthawi* ino,+

  • Miyambo 1:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Iyo imafuula kumapeto kwa misewu yaphokoso.+ Pazipata zolowera mumzinda, imanena mawu ake kuti:+

  • Yeremiya 19:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ukawauze kuti, ‘Tamverani mawu a Yehova inu mafumu a Yuda ndi inu okhala mu Yerusalemu.+ Yehova wa makamu,+ Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti:

      “‘“Ine ndikubweretsa tsoka pamalo ano, ndipo aliyense akadzamva za tsoka limeneli, makutu ake adzalira.+

  • Yeremiya 22:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ukanene kuti, ‘Tamverani mawu a Yehova, inu mfumu ya Yuda amene mwakhala pampando wachifumu wa Davide.+ Mumve mawu amenewa inuyo, atumiki anu komanso anthu anu amene amalowa pazipata izi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena